Yeremiya 49:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Mipanda ya Damasiko ndidzaiyatsa moto, ndipo motowo udzatentha nsanja zokhalamo za Beni-hadadi.”+ Amosi 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Yehova wanena kuti, ‘“Popeza kuti Damasiko+ anapanduka mobwerezabwereza,* sindidzamusinthira chigamulo changa. Sindidzamusinthira chigamulocho chifukwa chakuti anapuntha Giliyadi+ ndi zida zachitsulo zopunthira.
27 “Mipanda ya Damasiko ndidzaiyatsa moto, ndipo motowo udzatentha nsanja zokhalamo za Beni-hadadi.”+
3 “Yehova wanena kuti, ‘“Popeza kuti Damasiko+ anapanduka mobwerezabwereza,* sindidzamusinthira chigamulo changa. Sindidzamusinthira chigamulocho chifukwa chakuti anapuntha Giliyadi+ ndi zida zachitsulo zopunthira.