2 Mafumu 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 M’masiku ake, Farao Neko+ mfumu ya Iguputo inabwera kudzathandiza mfumu ya Asuri pamtsinje wa Firate,+ ndipo Mfumu Yosiya inapita kukamenyana ndi mfumu ya Iguputoyo,+ koma mfumuyo inapha Yosiya+ ku Megido+ itangomuona. 2 Mbiri 35:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Yosiya anapitabe kukakumana naye+ ndipo anadzisintha+ kuti amenyane naye. Iye sanamvere mawu a Neko+ ochokera pakamwa pa Mulungu. Choncho anapita kukamenyana naye m’chigwa cha Megido.+
29 M’masiku ake, Farao Neko+ mfumu ya Iguputo inabwera kudzathandiza mfumu ya Asuri pamtsinje wa Firate,+ ndipo Mfumu Yosiya inapita kukamenyana ndi mfumu ya Iguputoyo,+ koma mfumuyo inapha Yosiya+ ku Megido+ itangomuona.
22 Koma Yosiya anapitabe kukakumana naye+ ndipo anadzisintha+ kuti amenyane naye. Iye sanamvere mawu a Neko+ ochokera pakamwa pa Mulungu. Choncho anapita kukamenyana naye m’chigwa cha Megido.+