Salimo 75:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu opusa ndinawauza kuti: “Musakhale opusa,”+Ndipo oipa ndinawauza kuti: “Musakweze nyanga.*+ Salimo 110:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova amene ali kudzanja lako lamanja+Adzaphwanyaphwanya mafumu pa tsiku la mkwiyo wake.+ Luka 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Anthu adzaphedwa ndi lupanga ndiponso kutengedwa ukapolo kupita nawo ku mitundu ina yonse.+ Anthu a mitundu ina adzapondaponda Yerusalemu, kufikira nthawi zoikidwiratu+ za anthu a mitundu inawo zitakwanira.
24 Anthu adzaphedwa ndi lupanga ndiponso kutengedwa ukapolo kupita nawo ku mitundu ina yonse.+ Anthu a mitundu ina adzapondaponda Yerusalemu, kufikira nthawi zoikidwiratu+ za anthu a mitundu inawo zitakwanira.