Salimo 66:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti inu Mulungu mwatisanthula,+Mwatiyenga ngati siliva.+ Yesaya 48:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Taonani! Ndinakuyengani koma osati ngati mmene amayengera siliva.+ Ndinakusankhani pamene munali m’ng’anjo ya masautso.+ Malaki 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndani adzapirire pa tsiku limene adzabwere?+ Ndipo ndani adzaime chilili iye akadzaonekera?+ Iye adzakhala ngati moto wa woyenga zitsulo+ komanso ngati sopo+ wa ochapa zovala.+
10 Taonani! Ndinakuyengani koma osati ngati mmene amayengera siliva.+ Ndinakusankhani pamene munali m’ng’anjo ya masautso.+
2 “Ndani adzapirire pa tsiku limene adzabwere?+ Ndipo ndani adzaime chilili iye akadzaonekera?+ Iye adzakhala ngati moto wa woyenga zitsulo+ komanso ngati sopo+ wa ochapa zovala.+