Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 19:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Akatha, wansembeyo achape zovala zake n’kusamba thupi lake ndi madzi. Pambuyo pake akhoza kulowa mumsasa, koma akhalebe wodetsedwa mpaka madzulo.

  • Numeri 19:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 “‘Limeneli likhale lamulo mpaka kalekale kwa iwo, kuti munthu wowaza madzi oyeretsera, komanso munthu amene angakhudze madziwo, azichapa zovala zake.+ Akatero, azikhalabe wodetsedwa mpaka madzulo.

  • Hagai 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Choncho Hagai anati: “‘Umutu ndi mmene anthu awa alili, ndipo ndi mmene mtundu uwu wa anthu ulili pamaso panga.+ Ndi mmenenso ntchito yonse ya manja awo ndi chilichonse chimene amapereka nsembe chilili. Ndi zodetsedwa,’+ watero Yehova.

  • Chivumbulutso 3:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “‘Ngakhale zili choncho, uli ndi mayina+ angapo mu Sade a anthu amene sanaipitse+ malaya awo akunja. Amenewa adzayenda ndi ine atavala malaya oyera,+ chifukwa ndi oyenerera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena