Yeremiya 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti a m’nyumba ya Isiraeli ndi a m’nyumba ya Yuda andichitiradi zachinyengo,” watero Yehova.+ Hoseya 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Achitira Yehova zinthu zachinyengo,+ chifukwa abereka ana achilendo.+ Tsopano pomatha mwezi, iwo adzakhala atadyedwa limodzi ndi zinthu zawo.+ Malaki 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Kodi tonsefe atate wathu si mmodzi?+ Kodi si Mulungu mmodzi amene anatilenga?+ N’chifukwa chiyani tikuchitirana zachinyengo,+ mwa kuipitsa pangano la makolo athu akale?+
7 Achitira Yehova zinthu zachinyengo,+ chifukwa abereka ana achilendo.+ Tsopano pomatha mwezi, iwo adzakhala atadyedwa limodzi ndi zinthu zawo.+
10 “Kodi tonsefe atate wathu si mmodzi?+ Kodi si Mulungu mmodzi amene anatilenga?+ N’chifukwa chiyani tikuchitirana zachinyengo,+ mwa kuipitsa pangano la makolo athu akale?+