1 Mafumu 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ine ndakwanitsa kukumangirani nyumba yomwe ndi malo anu okhalamo okwezeka,+ malo okhazikika+ oti mukhalemo mpaka kalekale.”+ Salimo 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova ali m’kachisi wake wopatulika.+Yehova, mpando wake wachifumu uli kumwamba.+Maso ake amaona, maso ake owala amasanthula+ ana a anthu. Salimo 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova, ine ndimakonda nyumba imene inu mumakhala+Ndi malo amene kumakhala ulemerero wanu.+ Salimo 132:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Awa ndi malo anga okhalamo mpaka muyaya.+Ndidzakhala mmenemu, pakuti ndimafunitsitsa kukhala m’malo amenewa.+
13 Ine ndakwanitsa kukumangirani nyumba yomwe ndi malo anu okhalamo okwezeka,+ malo okhazikika+ oti mukhalemo mpaka kalekale.”+
4 Yehova ali m’kachisi wake wopatulika.+Yehova, mpando wake wachifumu uli kumwamba.+Maso ake amaona, maso ake owala amasanthula+ ana a anthu.
14 “Awa ndi malo anga okhalamo mpaka muyaya.+Ndidzakhala mmenemu, pakuti ndimafunitsitsa kukhala m’malo amenewa.+