Yesaya 53:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye ananyozedwa ndipo anthu anali kumupewa.+ Anali munthu amene anadziwa kupweteka ndiponso amene anadziwa matenda.+ Ife tinali kuyang’ana kumbali kuti tisaone nkhope yake.+ Ananyozedwa ndipo tinamuona ngati wopanda pake.+ Maliko 14:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Popita kumeneko anatenga Petulo, Yakobo ndi Yohane,+ ndipo anayamba kumva chisoni ndi kuvutika kwambiri mumtima mwake.+
3 Iye ananyozedwa ndipo anthu anali kumupewa.+ Anali munthu amene anadziwa kupweteka ndiponso amene anadziwa matenda.+ Ife tinali kuyang’ana kumbali kuti tisaone nkhope yake.+ Ananyozedwa ndipo tinamuona ngati wopanda pake.+
33 Popita kumeneko anatenga Petulo, Yakobo ndi Yohane,+ ndipo anayamba kumva chisoni ndi kuvutika kwambiri mumtima mwake.+