Oweruza 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 anali kumuuza kuti: “Nena kuti Shiboleti.”+ Koma iye anali kunena kuti: “Siboleti,” chifukwa sankatha kutchula mawuwa molondola. Akatero anali kumugwira ndi kumupha powolokera Yorodano pomwepo. Pa nthawi imeneyo panafa anthu 42,000 a ku Efuraimu.+ Luka 22:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Patapita pafupifupi ola lathunthu, munthu winanso anayamba kunena motsimikiza kuti: “Ndithu sindikukayika, munthu uyunso anali naye limodzi, ndipo iyeyu ndi Mgalileya!”+ Yohane 18:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mmodzi wa akapolo a mkulu wa ansembe, amenenso anali wachibale wa munthu amene Petulo anamudula khutu uja,+ anati: “Ndinakuona iwe m’munda muja uli naye limodzi, ndikunama kapena?”
6 anali kumuuza kuti: “Nena kuti Shiboleti.”+ Koma iye anali kunena kuti: “Siboleti,” chifukwa sankatha kutchula mawuwa molondola. Akatero anali kumugwira ndi kumupha powolokera Yorodano pomwepo. Pa nthawi imeneyo panafa anthu 42,000 a ku Efuraimu.+
59 Patapita pafupifupi ola lathunthu, munthu winanso anayamba kunena motsimikiza kuti: “Ndithu sindikukayika, munthu uyunso anali naye limodzi, ndipo iyeyu ndi Mgalileya!”+
26 Mmodzi wa akapolo a mkulu wa ansembe, amenenso anali wachibale wa munthu amene Petulo anamudula khutu uja,+ anati: “Ndinakuona iwe m’munda muja uli naye limodzi, ndikunama kapena?”