Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 26:73
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 73 Patapita kanthawi pang’ono, amene anali ataimirira chapafupi anabwera ndi kuuza Petulo kuti: “Ndithu iwenso uli m’gulu la ophunzira ake. Ndipo kalankhulidwe kako kakugwiritsa.”+

  • Maliko 14:70
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 70 Apanso anakana. Patapitanso kanthawi pang’ono, amene anali ataimirira chapafupi anayamba kuuza Petulo kuti: “Ndithu iwenso uli m’gulu la ophunzira ake. Ndipo ndiwenso Mgalileya.”+

  • Yohane 18:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Mmodzi wa akapolo a mkulu wa ansembe, amenenso anali wachibale wa munthu amene Petulo anamudula khutu uja,+ anati: “Ndinakuona iwe m’munda muja uli naye limodzi, ndikunama kapena?”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena