Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 14:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Ana anu adzakhala abusa m’chipululu+ kwa zaka 40, ndipo adzavutika chifukwa cha kusakhulupirika*+ kwanu, mpaka womalizira kufa wa inu atagona m’manda m’chipululu.+

  • Oweruza 19:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Mdzakazi wakeyo anakhala wosakhulupirika kwa iye, moti anayamba kuchita dama.+ Pamapeto pake, mkaziyo anachoka n’kukakhala kwa bambo ake ku Betelehemu wa ku Yuda miyezi inayi yathunthu.

  • Ezekieli 23:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Mng’ono wake Oholiba ataona zimenezi,+ anayamba kukonda chiwerewere chodziwononga nacho kuposa mkulu wake. Anayamba kuchita uhule kuposa dama la mkulu wake.+

  • Hoseya 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 popeza mayi wawo wachita dama.+ Mayi amene anatenga pakati kuti awabereke wachita zinthu zochititsa manyazi+ ndipo wanena kuti, ‘Ndikufuna kutsatira amene anali kundikonda kwambiri+ ndiponso amene anali kundipatsa chakudya, madzi, zovala za ubweya wa nkhosa, nsalu, mafuta ndi zakumwa.’+

  • Maliko 7:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pakuti mkatimo, mumtima mwa munthu,+ mumatuluka maganizo oipa. Mumatuluka zadama,*+ zakuba, zaumbanda,+

  • Machitidwe 5:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Poyankha Petulo ndi atumwi enawo ananena kuti: “Ife tiyenera kumvera Mulungu monga wolamulira, osati anthu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena