Mateyu 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Pamene mukusala kudya,+ lekani kumaonetsa nkhope yachisoni ngati mmene onyenga aja amachitira. Iwo amaipitsa nkhope zawo kuti aonekere kwa anthu kuti akusala kudya.+ Ndithu ndikukuuzani, Amenewo akulandiriratu mphoto yawo yonse. Mateyu 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zonse zimene amachita, amazichita kuti anthu awaone.+ Iwo amakulitsa timapukusi tokhala ndi malemba+ timene amavala monga zodzitetezera, ndipo amakulitsanso ulusi wopota wa m’mphepete+ mwa zovala zawo.
16 “Pamene mukusala kudya,+ lekani kumaonetsa nkhope yachisoni ngati mmene onyenga aja amachitira. Iwo amaipitsa nkhope zawo kuti aonekere kwa anthu kuti akusala kudya.+ Ndithu ndikukuuzani, Amenewo akulandiriratu mphoto yawo yonse.
5 Zonse zimene amachita, amazichita kuti anthu awaone.+ Iwo amakulitsa timapukusi tokhala ndi malemba+ timene amavala monga zodzitetezera, ndipo amakulitsanso ulusi wopota wa m’mphepete+ mwa zovala zawo.