Genesis 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Mulungu anati: “Dziko lapansi limere udzu, limere zomera zobala mbewu,+ limere mitengo yobala zipatso zokhala ndi mbewu yake, monga mwa mtundu wake.”+ Ndipo zinaterodi. Luka 6:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Pakuti mtengo uliwonse umadziwika ndi chipatso chake.+ Mwachitsanzo, anthu sathyola nkhuyu mumtengo waminga, kapena kudula mphesa m’chitsamba chaminga.+ Yakobo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Abale anga, kodi mkuyu ungabale maolivi, kapena mtengo wa mpesa ungabale nkhuyu?+ Ngakhale madzi amchere sangatulutse madzi abwino.
11 Ndiyeno Mulungu anati: “Dziko lapansi limere udzu, limere zomera zobala mbewu,+ limere mitengo yobala zipatso zokhala ndi mbewu yake, monga mwa mtundu wake.”+ Ndipo zinaterodi.
44 Pakuti mtengo uliwonse umadziwika ndi chipatso chake.+ Mwachitsanzo, anthu sathyola nkhuyu mumtengo waminga, kapena kudula mphesa m’chitsamba chaminga.+
12 Abale anga, kodi mkuyu ungabale maolivi, kapena mtengo wa mpesa ungabale nkhuyu?+ Ngakhale madzi amchere sangatulutse madzi abwino.