Maliko 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho iye anailola. Pamenepo mizimu yonyansayo inatuluka ndi kukalowa m’nkhumbazo, ndipo nkhumba zonsezo zinathamangira kuphedi ndi kulumphira m’nyanja. Nkhumbazo zinalipo pafupifupi 2,000, ndipo zinamira m’nyanjamo imodzi ndi imodzi.+ Luka 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Choncho ziwandazo zinatuluka mwa munthuyo ndi kukalowa munkhumbazo. Pamenepo nkhumba zonsezo zinathamangira kuphedi ndi kulumphira m’nyanja ndipo zinamira.+
13 Choncho iye anailola. Pamenepo mizimu yonyansayo inatuluka ndi kukalowa m’nkhumbazo, ndipo nkhumba zonsezo zinathamangira kuphedi ndi kulumphira m’nyanja. Nkhumbazo zinalipo pafupifupi 2,000, ndipo zinamira m’nyanjamo imodzi ndi imodzi.+
33 Choncho ziwandazo zinatuluka mwa munthuyo ndi kukalowa munkhumbazo. Pamenepo nkhumba zonsezo zinathamangira kuphedi ndi kulumphira m’nyanja ndipo zinamira.+