Mateyu 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pamenepo iye anaziuza kuti: “Pitani!” Choncho zinatuluka ndi kukalowa m’nkhumba zija. Nthawi yomweyo nkhumba zonsezo zinathamangira kuphedi ndi kulumphira m’nyanja, ndipo zinafera m’madzimo.+ Maliko 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho iye anailola. Pamenepo mizimu yonyansayo inatuluka ndi kukalowa m’nkhumbazo, ndipo nkhumba zonsezo zinathamangira kuphedi ndi kulumphira m’nyanja. Nkhumbazo zinalipo pafupifupi 2,000, ndipo zinamira m’nyanjamo imodzi ndi imodzi.+
32 Pamenepo iye anaziuza kuti: “Pitani!” Choncho zinatuluka ndi kukalowa m’nkhumba zija. Nthawi yomweyo nkhumba zonsezo zinathamangira kuphedi ndi kulumphira m’nyanja, ndipo zinafera m’madzimo.+
13 Choncho iye anailola. Pamenepo mizimu yonyansayo inatuluka ndi kukalowa m’nkhumbazo, ndipo nkhumba zonsezo zinathamangira kuphedi ndi kulumphira m’nyanja. Nkhumbazo zinalipo pafupifupi 2,000, ndipo zinamira m’nyanjamo imodzi ndi imodzi.+