Mateyu 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pamenepo iye anaziuza kuti: “Pitani!” Choncho zinatuluka ndi kukalowa m’nkhumba zija. Nthawi yomweyo nkhumba zonsezo zinathamangira kuphedi ndi kulumphira m’nyanja, ndipo zinafera m’madzimo.+ Luka 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Choncho ziwandazo zinatuluka mwa munthuyo ndi kukalowa munkhumbazo. Pamenepo nkhumba zonsezo zinathamangira kuphedi ndi kulumphira m’nyanja ndipo zinamira.+
32 Pamenepo iye anaziuza kuti: “Pitani!” Choncho zinatuluka ndi kukalowa m’nkhumba zija. Nthawi yomweyo nkhumba zonsezo zinathamangira kuphedi ndi kulumphira m’nyanja, ndipo zinafera m’madzimo.+
33 Choncho ziwandazo zinatuluka mwa munthuyo ndi kukalowa munkhumbazo. Pamenepo nkhumba zonsezo zinathamangira kuphedi ndi kulumphira m’nyanja ndipo zinamira.+