Maliko 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno anasankha gulu la anthu 12, amenenso anawatcha “atumwi,” kuti azikhala naye nthawi zonse ndi kuti aziwatuma kukalalikira+ Maliko 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 ndi kuwapatsa mphamvu zotulutsa ziwanda.+ Maliko 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako anaitana ophunzira 12 aja, ndipo anayamba kuwatumiza awiriawiri,+ ndi kuwapatsa mphamvu pa mizimu yonyansa.+ Luka 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano Yesu anasonkhanitsa atumwi 12 aja ndi kuwapatsa mphamvu ndi ulamuliro pa ziwanda zonse ndi kuti azitha kuchiritsa matenda.+
14 Ndiyeno anasankha gulu la anthu 12, amenenso anawatcha “atumwi,” kuti azikhala naye nthawi zonse ndi kuti aziwatuma kukalalikira+
7 Kenako anaitana ophunzira 12 aja, ndipo anayamba kuwatumiza awiriawiri,+ ndi kuwapatsa mphamvu pa mizimu yonyansa.+
9 Tsopano Yesu anasonkhanitsa atumwi 12 aja ndi kuwapatsa mphamvu ndi ulamuliro pa ziwanda zonse ndi kuti azitha kuchiritsa matenda.+