Mateyu 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndithu ndikukuuzani, Chilango cha Sodomu+ ndi Gomora pa Tsiku la Chiweruzo chidzakhala chocheperako poyerekeza ndi cha mzinda umenewo.+ Mateyu 12:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Anthu a ku Nineve adzaimirira pa chiweruzo limodzi ndi m’badwo uwu+ ndipo adzautsutsa,+ chifukwa iwo analapa atamva ulaliki wa Yona.+ Koma tsopano wina woposa Yona ali pano. Luka 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndithu ndikukuuzani, chilango cha Sodomu+ pa tsiku limenelo chidzakhala chocheperako poyerekeza ndi cha mzinda umenewo.
15 Ndithu ndikukuuzani, Chilango cha Sodomu+ ndi Gomora pa Tsiku la Chiweruzo chidzakhala chocheperako poyerekeza ndi cha mzinda umenewo.+
41 Anthu a ku Nineve adzaimirira pa chiweruzo limodzi ndi m’badwo uwu+ ndipo adzautsutsa,+ chifukwa iwo analapa atamva ulaliki wa Yona.+ Koma tsopano wina woposa Yona ali pano.
12 Ndithu ndikukuuzani, chilango cha Sodomu+ pa tsiku limenelo chidzakhala chocheperako poyerekeza ndi cha mzinda umenewo.