Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliro 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Chilango chimene mwana wamkazi wa anthu anga walandira chifukwa cha zolakwa zake, n’chachikulu kuposa chimene mzinda wa Sodomu unalandira chifukwa cha machimo ake.+

      Mzinda umenewu unawonongedwa mwadzidzidzi m’kanthawi kochepa, ndipo palibe dzanja limene linauthandiza.+

  • Ezekieli 16:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Pali ine Mulungu wamoyo, m’bale wako Sodomu ndi midzi yake yozungulira, sanachite mofanana ndi zimene iwe ndi midzi yako yozungulira munachita,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.

  • Mateyu 11:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Koma tsopano ndikukuuzani anthu inu kuti, Chilango cha Sodomu pa Tsiku la Chiweruzo chidzakhala chocheperako poyerekeza ndi cha Kaperenao.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena