1 Samueli 14:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pamenepo mmodzi mwa anthuwo anamuuza kuti: “Bambo ako alumbirira anthu kuti, ‘Munthu aliyense wodya mkate lero ndi wotembereredwa!’”+ (Apa n’kuti anthuwo atayamba kutopa.)+ 1 Samueli 25:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho Mulungu alange mowirikiza+ adani a Davide, ngati ine ndidzasiya munthu aliyense wa m’nyumba ya Nabala wokodzera khoma*+ ali wamoyo kufikira m’mawa.”+ Maliko 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo mwana wamkazi wa Herodiya analowa ndi kuvina, moti anasangalatsa Herode ndi ena amene anali kudya+ naye limodzi. Tsopano mfumu inauza mtsikanayo kuti: “Upemphe kwa ine chilichonse chimene ukufuna, ndipo ndidzakupatsa.”
28 Pamenepo mmodzi mwa anthuwo anamuuza kuti: “Bambo ako alumbirira anthu kuti, ‘Munthu aliyense wodya mkate lero ndi wotembereredwa!’”+ (Apa n’kuti anthuwo atayamba kutopa.)+
22 Choncho Mulungu alange mowirikiza+ adani a Davide, ngati ine ndidzasiya munthu aliyense wa m’nyumba ya Nabala wokodzera khoma*+ ali wamoyo kufikira m’mawa.”+
22 Ndipo mwana wamkazi wa Herodiya analowa ndi kuvina, moti anasangalatsa Herode ndi ena amene anali kudya+ naye limodzi. Tsopano mfumu inauza mtsikanayo kuti: “Upemphe kwa ine chilichonse chimene ukufuna, ndipo ndidzakupatsa.”