Genesis 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Mulungu anati: “Dziko lapansi limere udzu, limere zomera zobala mbewu,+ limere mitengo yobala zipatso zokhala ndi mbewu yake, monga mwa mtundu wake.”+ Ndipo zinaterodi. Agalatiya 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musanyengedwe,+ Mulungu sapusitsika.+ Chilichonse chimene munthu wafesa, adzakololanso chomwecho.+
11 Ndiyeno Mulungu anati: “Dziko lapansi limere udzu, limere zomera zobala mbewu,+ limere mitengo yobala zipatso zokhala ndi mbewu yake, monga mwa mtundu wake.”+ Ndipo zinaterodi.