Mateyu 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Musachite mantha+ ndi amene amapha thupi koma sangaphe moyo, m’malomwake, muziopa iye+ amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe m’Gehena.*+ Mateyu 23:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Njoka inu, ana a mphiri,+ mudzathawa bwanji chiweruzo cha Gehena?+ Luka 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ndikuuzani woti muzimuopa: Muziopa iye+ amene amati akapha, amakhalanso ndi mphamvu zoponya munthu m’Gehena.*+ Ndithu ndikukuuzani, muziopa+ Ameneyu.
28 Musachite mantha+ ndi amene amapha thupi koma sangaphe moyo, m’malomwake, muziopa iye+ amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe m’Gehena.*+
5 Koma ndikuuzani woti muzimuopa: Muziopa iye+ amene amati akapha, amakhalanso ndi mphamvu zoponya munthu m’Gehena.*+ Ndithu ndikukuuzani, muziopa+ Ameneyu.