Salimo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndinene za lamulo la Yehova.Iye wandiuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga,+Lero, ine ndakhala bambo ako.+ Mateyu 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Tamverani! Namwali+ adzatenga pakati ndipo adzabereka mwana wamwamuna. Mwanayo adzam’patsa dzina lakuti Emanueli,”+ lotanthauza “Mulungu Ali Nafe,”+ likamasuliridwa. Agalatiya 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma nthawi itakwana,+ Mulungu anatumiza Mwana wake,+ amene anadzabadwa kwa mkazi+ ndipo anadzakhala pansi pa chilamulo.+ 1 Yohane 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mulungu anatisonyeza ife chikondi chake+ pakuti anatumiza m’dziko Mwana wake wobadwa yekha+ kuti tipeze moyo kudzera mwa iye.+
7 Ndinene za lamulo la Yehova.Iye wandiuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga,+Lero, ine ndakhala bambo ako.+
23 “Tamverani! Namwali+ adzatenga pakati ndipo adzabereka mwana wamwamuna. Mwanayo adzam’patsa dzina lakuti Emanueli,”+ lotanthauza “Mulungu Ali Nafe,”+ likamasuliridwa.
4 Koma nthawi itakwana,+ Mulungu anatumiza Mwana wake,+ amene anadzabadwa kwa mkazi+ ndipo anadzakhala pansi pa chilamulo.+
9 Mulungu anatisonyeza ife chikondi chake+ pakuti anatumiza m’dziko Mwana wake wobadwa yekha+ kuti tipeze moyo kudzera mwa iye.+