Mateyu 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumeneko anthu anam’bweretsera munthu wakufa ziwalo, atagona pakabedi.+ Poona chikhulupiriro chawo, Yesu anauza wakufa ziwaloyo kuti: “Limba mtima, mwanawe, machimo ako akhululukidwa.”+ Luka 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako panafika anthu atanyamula munthu wakufa ziwalo pakabedi. Iwo anali kufunafuna njira yoti amulowetsere ndi kumuika pafupi ndi Yesu.+
2 Kumeneko anthu anam’bweretsera munthu wakufa ziwalo, atagona pakabedi.+ Poona chikhulupiriro chawo, Yesu anauza wakufa ziwaloyo kuti: “Limba mtima, mwanawe, machimo ako akhululukidwa.”+
18 Kenako panafika anthu atanyamula munthu wakufa ziwalo pakabedi. Iwo anali kufunafuna njira yoti amulowetsere ndi kumuika pafupi ndi Yesu.+