Mateyu 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Chotero makamu a anthu ambiri ochokera ku Galileya,+ ku Dekapole, ku Yerusalemu,+ ku Yudeya komanso ochokera kutsidya lina la Yorodano, anam’tsatira. Maliko 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Yesu ndi ophunzira ake anachoka ndi kupita kunyanja. Chikhamu cha anthu ochokera ku Galileya ndi ku Yudeya chinam’tsatira.+ Yohane 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma khamu lalikulu la anthu linali kumutsatira, chifukwa linali kuona zizindikiro zimene iye anali kuchita pa odwala.+
25 Chotero makamu a anthu ambiri ochokera ku Galileya,+ ku Dekapole, ku Yerusalemu,+ ku Yudeya komanso ochokera kutsidya lina la Yorodano, anam’tsatira.
7 Koma Yesu ndi ophunzira ake anachoka ndi kupita kunyanja. Chikhamu cha anthu ochokera ku Galileya ndi ku Yudeya chinam’tsatira.+
2 Koma khamu lalikulu la anthu linali kumutsatira, chifukwa linali kuona zizindikiro zimene iye anali kuchita pa odwala.+