Salimo 65:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye akutontholetsa phokoso la nyanja,+Akutontholetsa phokoso la mafunde ake komanso chipwirikiti cha mitundu ya anthu.+ Mateyu 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma iye anawafunsa kuti: “N’chifukwa chiyani mukuchita mantha chonchi, anthu achikhulupiriro chochepa inu?”+ Kenako anadzuka n’kudzudzula mphepo ndi nyanjayo, ndipo panachita bata lalikulu.+ Maliko 4:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Pamenepo anadzuka ndi kudzudzula mphepoyo ndi kuuza nyanjayo kuti: “Leka! Khala bata!”+ Chotero mphepoyo inaleka. Kenako panachita bata lalikulu.+
7 Iye akutontholetsa phokoso la nyanja,+Akutontholetsa phokoso la mafunde ake komanso chipwirikiti cha mitundu ya anthu.+
26 Koma iye anawafunsa kuti: “N’chifukwa chiyani mukuchita mantha chonchi, anthu achikhulupiriro chochepa inu?”+ Kenako anadzuka n’kudzudzula mphepo ndi nyanjayo, ndipo panachita bata lalikulu.+
39 Pamenepo anadzuka ndi kudzudzula mphepoyo ndi kuuza nyanjayo kuti: “Leka! Khala bata!”+ Chotero mphepoyo inaleka. Kenako panachita bata lalikulu.+