Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 9:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Anthu amene anali kuyenda mu mdima, aona kuwala kwakukulu.+ Anthu amene anali kukhala m’dziko la mdima wandiweyani,+ kuwala kwawawalira.+

  • Yesaya 49:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno iye anati: “Si nkhani yochepa kuti iweyo wakhala mtumiki wanga, n’cholinga choti ubwezeretse mafuko a Yakobo ndi kubweza Aisiraeli amene ali otetezeka.+ Ndakupereka kuti ukhale kuwala kwa mitundu ya anthu,+ kuti chipulumutso changa chifike mpaka kumalekezero a dziko lapansi.”+

  • Mateyu 4:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 anthu okhala mu mdima+ anaona kuwala kwakukulu,+ ndipo anthu okhala m’dera la mthunzi wa imfa, kuwala+ kunawatulukira.”+

  • Yohane 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kuwalako kukuunika mumdima,+ ndipo mdimawo sunagonjetse kuwalako.

  • Yohane 12:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Pamenepo Yesu anati: “Kuwala kukhalabe pakati panu kanthawi pang’ono. Yendani pamene kuwalako mudakali nako, kuti mdima+ usakugwereni, pakuti woyenda mu mdima sadziwa kumene akupita.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena