Mateyu 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Atate wanga wapereka zinthu zonse kwa ine, ndipo palibe amene akum’dziwa bwino Mwana koma Atate+ okha, komanso palibe amene akuwadziwa bwino Atate koma Mwana yekha+ ndi aliyense amene Mwanayo wafuna kumuululira za Atatewo.+ Yohane 8:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 chikhalirecho simukumudziwa.+ Koma ine ndikumudziwa.+ Ngati ndinganene kuti sindikumudziwa ndingakhale wabodza, kufanana ndi inuyo. Koma ndikumudziwa ndithu ndipo ndikusunga mawu ake.+ Yohane 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma adzakuchitirani zonsezi chifukwa cha dzina langa, chifukwa amene anandituma ine sakumudziwa.+
27 Atate wanga wapereka zinthu zonse kwa ine, ndipo palibe amene akum’dziwa bwino Mwana koma Atate+ okha, komanso palibe amene akuwadziwa bwino Atate koma Mwana yekha+ ndi aliyense amene Mwanayo wafuna kumuululira za Atatewo.+
55 chikhalirecho simukumudziwa.+ Koma ine ndikumudziwa.+ Ngati ndinganene kuti sindikumudziwa ndingakhale wabodza, kufanana ndi inuyo. Koma ndikumudziwa ndithu ndipo ndikusunga mawu ake.+
21 Koma adzakuchitirani zonsezi chifukwa cha dzina langa, chifukwa amene anandituma ine sakumudziwa.+