Mateyu 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nthawi yomweyo iwo anafuula, kuti: “Kodi tili nanu chiyani, Mwana wa Mulungu?+ Kodi mwabwera kudzatizunza+ nthawi yoikidwiratu isanakwane?”+ Maliko 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 kuti: “Kodi tili nanu chiyani, Yesu Mnazareti?+ Kodi mwabwera kudzatiwononga? Inetu ndikukudziwani+ bwino kwambiri, ndinu Woyera+ wa Mulungu.”+ Luka 4:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Tili nanu chiyani,+ Yesu Mnazareti?+ Kodi mwabwera kudzatiwononga? Inetu ndikukudziwani+ bwino kwambiri, ndinu Woyera wa Mulungu.”+
29 Nthawi yomweyo iwo anafuula, kuti: “Kodi tili nanu chiyani, Mwana wa Mulungu?+ Kodi mwabwera kudzatizunza+ nthawi yoikidwiratu isanakwane?”+
24 kuti: “Kodi tili nanu chiyani, Yesu Mnazareti?+ Kodi mwabwera kudzatiwononga? Inetu ndikukudziwani+ bwino kwambiri, ndinu Woyera+ wa Mulungu.”+
34 “Tili nanu chiyani,+ Yesu Mnazareti?+ Kodi mwabwera kudzatiwononga? Inetu ndikukudziwani+ bwino kwambiri, ndinu Woyera wa Mulungu.”+