Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Akorinto 6:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kodi zoonadi inu simukudziwa kuti anthu osalungama sadzalowa mu ufumu wa Mulungu?+ Musasocheretsedwe. Adama,+ opembedza mafano,+ achigololo,+ amuna amene amagonedwa ndi amuna anzawo,+ amuna ogona amuna anzawo,+

  • Akolose 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Choncho chititsani ziwalo za thupi+ lanu padziko lapansi kukhala zakufa+ ku dama, zinthu zodetsa, chilakolako cha kugonana,+ chikhumbo choipa, ndi kusirira kwa nsanje,+ kumene ndiko kulambira mafano.

  • 1 Atesalonika 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mulungu akufuna kuti mukhale oyera+ mwa kupewa dama.*+

  • 1 Petulo 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pakuti nthawi+ imene yapitayi inali yokwanira kwa inu kuchita chifuniro cha anthu a m’dzikoli+ pamene munali kuchita zinthu zosonyeza khalidwe lotayirira,+ zilakolako zoipa, kumwa vinyo mopitirira muyezo,+ maphwando aphokoso, kumwa kwa mpikisano, ndi kupembedza mafano kosaloleka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena