Mateyu 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inetu ndikukubatizani m’madzi+ chifukwa cha kulapa kwanu,+ koma amene akubwera+ m’mbuyo mwanga ndi wamphamvu kuposa ine, ndipo sindili woyenera kumuvula nsapato zake.+ Ameneyo adzakubatizani ndi mzimu woyera+ komanso ndi moto.+ Machitidwe 8:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Akuyenda choncho mumsewumo, anapeza madzi ambiri, ndipo nduna ija inati: “Taonani! Si awa madzi ambiri. Chikundiletsa kubatizidwa n’chiyani?”+ Machitidwe 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chotero ngati Mulungu anapereka mphatso yaulere imodzimodziyo kwa iwo, monga mmenenso anachitira kwa ife amene tinakhulupirira mwa Ambuye Yesu Khristu,+ ine ndine ndani kuti ndiletse Mulungu?”+
11 Inetu ndikukubatizani m’madzi+ chifukwa cha kulapa kwanu,+ koma amene akubwera+ m’mbuyo mwanga ndi wamphamvu kuposa ine, ndipo sindili woyenera kumuvula nsapato zake.+ Ameneyo adzakubatizani ndi mzimu woyera+ komanso ndi moto.+
36 Akuyenda choncho mumsewumo, anapeza madzi ambiri, ndipo nduna ija inati: “Taonani! Si awa madzi ambiri. Chikundiletsa kubatizidwa n’chiyani?”+
17 Chotero ngati Mulungu anapereka mphatso yaulere imodzimodziyo kwa iwo, monga mmenenso anachitira kwa ife amene tinakhulupirira mwa Ambuye Yesu Khristu,+ ine ndine ndani kuti ndiletse Mulungu?”+