Aroma 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 ndili ndi chikhulupiriro kuti mulimonse mmene zingakhalire, pa ulendo wanga wa ku Sipaniya+ nthawi ina iliyonse, ndidzaonana nanu. Ndikadzacheza nanu mpaka kukhutira, mudzandiperekeza+ pa ulendo wangawo. 1 Akorinto 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwina ndidzakhala nanu pang’ono kumeneko, ngakhalenso kwa nyengo yonse yachisanu, kuti mudzandiperekeze+ kumene ndizidzapitako.
24 ndili ndi chikhulupiriro kuti mulimonse mmene zingakhalire, pa ulendo wanga wa ku Sipaniya+ nthawi ina iliyonse, ndidzaonana nanu. Ndikadzacheza nanu mpaka kukhutira, mudzandiperekeza+ pa ulendo wangawo.
6 Mwina ndidzakhala nanu pang’ono kumeneko, ngakhalenso kwa nyengo yonse yachisanu, kuti mudzandiperekeze+ kumene ndizidzapitako.