Machitidwe 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo anthu amene anaperekeza Paulo anakamufikitsa ku Atene. Koma anabwerera atatumidwa kuti akauze Sila ndi Timoteyo+ kuti amutsatire msanga. Aroma 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 ndili ndi chikhulupiriro kuti mulimonse mmene zingakhalire, pa ulendo wanga wa ku Sipaniya+ nthawi ina iliyonse, ndidzaonana nanu. Ndikadzacheza nanu mpaka kukhutira, mudzandiperekeza+ pa ulendo wangawo. 3 Yohane 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Abalewo achitira umboni ku mpingo za chikondi chako. Anthu oterewa akamachoka, utsanzikane nawo m’njira imene Mulungu angasangalale nayo,+
15 Ndipo anthu amene anaperekeza Paulo anakamufikitsa ku Atene. Koma anabwerera atatumidwa kuti akauze Sila ndi Timoteyo+ kuti amutsatire msanga.
24 ndili ndi chikhulupiriro kuti mulimonse mmene zingakhalire, pa ulendo wanga wa ku Sipaniya+ nthawi ina iliyonse, ndidzaonana nanu. Ndikadzacheza nanu mpaka kukhutira, mudzandiperekeza+ pa ulendo wangawo.
6 Abalewo achitira umboni ku mpingo za chikondi chako. Anthu oterewa akamachoka, utsanzikane nawo m’njira imene Mulungu angasangalale nayo,+