Machitidwe 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano mpingo utawaperekeza,+ amuna amenewa anapitiriza ulendo wawo kudzera ku Foinike ndi ku Samariya. Kumeneko anali kufotokoza mwatsatanetsatane za kutembenuka kwa anthu a mitundu ina,+ ndipo iwo anasangalatsa kwambiri abale onse.+ 1 Akorinto 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwina ndidzakhala nanu pang’ono kumeneko, ngakhalenso kwa nyengo yonse yachisanu, kuti mudzandiperekeze+ kumene ndizidzapitako.
3 Tsopano mpingo utawaperekeza,+ amuna amenewa anapitiriza ulendo wawo kudzera ku Foinike ndi ku Samariya. Kumeneko anali kufotokoza mwatsatanetsatane za kutembenuka kwa anthu a mitundu ina,+ ndipo iwo anasangalatsa kwambiri abale onse.+
6 Mwina ndidzakhala nanu pang’ono kumeneko, ngakhalenso kwa nyengo yonse yachisanu, kuti mudzandiperekeze+ kumene ndizidzapitako.