Yohane 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mthandiziyo akadzafika, amene ndi mzimu wa choonadi,+ adzakutsogolerani m’choonadi chonse. Pakuti sadzalankhula zongoganiza mwa iye yekha, koma adzalankhula zimene wazimva, ndipo adzalengeza kwa inu zinthu zimene zikubwera.+ Machitidwe 5:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndipo ife ndife mboni za zinthu zimenezi,+ chimodzimodzinso mzimu woyera,+ umene Mulungu wapereka kwa anthu omumvera monga wolamulira.”
13 Koma mthandiziyo akadzafika, amene ndi mzimu wa choonadi,+ adzakutsogolerani m’choonadi chonse. Pakuti sadzalankhula zongoganiza mwa iye yekha, koma adzalankhula zimene wazimva, ndipo adzalengeza kwa inu zinthu zimene zikubwera.+
32 Ndipo ife ndife mboni za zinthu zimenezi,+ chimodzimodzinso mzimu woyera,+ umene Mulungu wapereka kwa anthu omumvera monga wolamulira.”