Machitidwe 18:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mwamuna ameneyu anayamba kulankhula molimba mtima musunagoge. Tsopano Purisikila ndi Akula+ atamumvetsera, anamutenga ndi kumufotokozera njira ya Mulungu molondola. 1 Akorinto 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mipingo ya ku Asia ikupereka moni.+ Akula ndi Purisika, pamodzi ndi mpingo umene umasonkhana m’nyumba mwawo,+ akupereka moni wochokera pansi pa mtima kwa inu nonse, mwa Ambuye. 2 Timoteyo 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Undiperekere moni kwa Purisika+ ndi Akula, ndi banja la Onesiforo.+
26 Mwamuna ameneyu anayamba kulankhula molimba mtima musunagoge. Tsopano Purisikila ndi Akula+ atamumvetsera, anamutenga ndi kumufotokozera njira ya Mulungu molondola.
19 Mipingo ya ku Asia ikupereka moni.+ Akula ndi Purisika, pamodzi ndi mpingo umene umasonkhana m’nyumba mwawo,+ akupereka moni wochokera pansi pa mtima kwa inu nonse, mwa Ambuye.