Aroma 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mundiperekere moni kwa Purisika ndi Akula,+ antchito anzanga+ mwa Khristu Yesu. 1 Akorinto 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mipingo ya ku Asia ikupereka moni.+ Akula ndi Purisika, pamodzi ndi mpingo umene umasonkhana m’nyumba mwawo,+ akupereka moni wochokera pansi pa mtima kwa inu nonse, mwa Ambuye.
19 Mipingo ya ku Asia ikupereka moni.+ Akula ndi Purisika, pamodzi ndi mpingo umene umasonkhana m’nyumba mwawo,+ akupereka moni wochokera pansi pa mtima kwa inu nonse, mwa Ambuye.