Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 18:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kumeneko anapeza Myuda wina dzina lake Akula,+ mbadwa ya ku Ponto. Iyeyu pamodzi ndi mkazi wake Purisikila, anali atafika chaposachedwa kuchokera ku Italiya,+ chifukwa Kalaudiyo+ anali atalamula Ayuda onse kuti achoke ku Roma. Choncho Paulo anapita kwa iwo.

  • Machitidwe 18:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Mwamuna ameneyu anayamba kulankhula molimba mtima musunagoge. Tsopano Purisikila ndi Akula+ atamumvetsera, anamutenga ndi kumufotokozera njira ya Mulungu molondola.

  • 1 Akorinto 16:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mipingo ya ku Asia ikupereka moni.+ Akula ndi Purisika, pamodzi ndi mpingo umene umasonkhana m’nyumba mwawo,+ akupereka moni wochokera pansi pa mtima kwa inu nonse, mwa Ambuye.

  • 2 Timoteyo 4:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Undiperekere moni kwa Purisika+ ndi Akula, ndi banja la Onesiforo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena