Salimo 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye adzaweruza anthu padziko lapansi mwachilungamo.+Adzazenga mlandu mitundu ya anthu moyenerera.+ Salimo 96:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti iye wabwera.+Iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu mokhulupirika.+ Salimo 98:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu molungama.+ Machitidwe 17:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ m’chilungamo dziko lapansi kumene kuli anthu, kudzera mwa munthu amene iye wamuika. Ndipo wapereka chitsimikizo kwa anthu onse mwa kumuukitsa+ kwa akufa.”
13 Pakuti iye wabwera.+Iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu mokhulupirika.+
9 Pakuti iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu molungama.+
31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ m’chilungamo dziko lapansi kumene kuli anthu, kudzera mwa munthu amene iye wamuika. Ndipo wapereka chitsimikizo kwa anthu onse mwa kumuukitsa+ kwa akufa.”