Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 5:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense wothetsa ukwati ndi mkazi wake, osati chifukwa cha dama,*+ amamuchititsa chigololo akakwatiwanso,+ ndipo aliyense wokwatira mkazi wosiyidwayo nayenso wachita chigololo.+

  • Mateyu 19:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ine ndikukuuzani kuti aliyense wosiya mkazi wake n’kukwatira wina wachita chigololo, kupatulapo ngati wamusiya chifukwa cha dama.”*+

  • Maliko 10:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndipo ngati mkazi wasiya mwamuna wake, ndiyeno n’kukwatiwa ndi wina, wachita chigololo.”+

  • Luka 16:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Aliyense wosiya mkazi wake ndi kukwatira wina, wachita chigololo, ndipo wokwatira mkazi wosiyidwayo wachita chigololo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena