Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Malaki 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Inu mwanena kuti, ‘Chifukwa chiyani?’+ Chifukwa chakuti Yehova wakudzudzulani popeza kuti aliyense wa inu wachitira zachinyengo mkazi amene anamukwatira ali mnyamata,+ ngakhale kuti iye anali mnzake komanso mkazi wa pangano lake.+

  • Mateyu 5:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense wothetsa ukwati ndi mkazi wake, osati chifukwa cha dama,*+ amamuchititsa chigololo akakwatiwanso,+ ndipo aliyense wokwatira mkazi wosiyidwayo nayenso wachita chigololo.+

  • Maliko 10:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iye anawauza kuti: “Aliyense wosiya mkazi wake ndi kukwatira wina, wachita chigololo+ molakwira mkaziyo.

  • Luka 16:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Aliyense wosiya mkazi wake ndi kukwatira wina, wachita chigololo, ndipo wokwatira mkazi wosiyidwayo wachita chigololo.+

  • Aroma 7:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ngati angakwatiwe ndi mwamuna wina, mwamuna wake ali moyo, mkaziyo adzatchedwa wachigololo.+ Koma ngati mwamuna wake wamwalira, mkaziyo wamasuka ku lamulo lake, chotero si wachigololo ngati atakwatiwa ndi mwamuna wina.+

  • 1 Akorinto 7:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kwa okwatira ndikupereka malangizo awa, kwenikweni osati ineyo koma Ambuye,+ kuti mkazi asasiye mwamuna wake,+

  • Aheberi 13:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ukwati ukhale wolemekezeka kwa onse, ndipo pogona pa anthu okwatirana pakhale posaipitsidwa,+ pakuti Mulungu adzaweruza adama ndi achigololo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena