Akolose 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 tsopano wagwirizana+ nanunso pogwiritsa ntchito thupi lanyama la mwanayo kudzera mu imfa yake.+ Wachita izi kuti akuperekeni pamaso pa iyeyo, muli opatulika ndi opanda chilema,+ ndiponso opanda chifukwa chokunenezerani.+ 1 Yohane 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Komanso, munthu wosunga malamulo ake amakhalabe wogwirizana naye.+ Iyenso amakhala wogwirizana ndi munthuyo, ndipo chifukwa cha mzimu+ umene anatipatsa, timadziwa kuti ndife ogwirizana naye.+
22 tsopano wagwirizana+ nanunso pogwiritsa ntchito thupi lanyama la mwanayo kudzera mu imfa yake.+ Wachita izi kuti akuperekeni pamaso pa iyeyo, muli opatulika ndi opanda chilema,+ ndiponso opanda chifukwa chokunenezerani.+
24 Komanso, munthu wosunga malamulo ake amakhalabe wogwirizana naye.+ Iyenso amakhala wogwirizana ndi munthuyo, ndipo chifukwa cha mzimu+ umene anatipatsa, timadziwa kuti ndife ogwirizana naye.+