Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 5:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Pakuti inu sindinu Mulungu wokondwera ndi zoipa,+

      Palibe munthu woipa amene angakhale ndi inu ngakhale kwa kanthawi kochepa.+

  • Yesaya 59:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ayi si choncho. Koma zolakwa za anthu inu n’zimene zakulekanitsani ndi Mulungu wanu,+ ndipo machimo anu amuchititsa kuti akubisireni nkhope yake, kuti asamve zimene mukunena.+

  • Akolose 1:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndithudi, inu amene kale munali otalikirana+ naye ndiponso adani ake chifukwa maganizo anu anali pa ntchito zoipa,+

  • Yakobo 4:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Achigololo+ inu, kodi simukudziwa kuti kuchita ubwenzi ndi dziko n’kudziika pa udani ndi Mulungu?+ Choncho, aliyense amene akufuna kukhala bwenzi+ la dziko akudzisandutsa mdani wa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena