Yesaya 60:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anthu ako onse adzakhala olungama.+ Iwo adzakhala m’dzikomo mpaka kalekale.+ Anthuwo adzakhala mmera wobzalidwa ndi ine+ ndiponso ntchito ya manja anga,+ kuti ineyo ndikongoletsedwe.+ Aheberi 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti onse, woyeretsayo ndi amene akuyeretsedwawo,+ amachokera kwa mmodzi.+ Pa chifukwa chimenechi, iye sachita manyazi kuwatcha “abale,”+
21 Anthu ako onse adzakhala olungama.+ Iwo adzakhala m’dzikomo mpaka kalekale.+ Anthuwo adzakhala mmera wobzalidwa ndi ine+ ndiponso ntchito ya manja anga,+ kuti ineyo ndikongoletsedwe.+
11 Pakuti onse, woyeretsayo ndi amene akuyeretsedwawo,+ amachokera kwa mmodzi.+ Pa chifukwa chimenechi, iye sachita manyazi kuwatcha “abale,”+