1 Akorinto 1:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 kuti zikhale monga Malemba amanenera kuti: “Amene akudzitama, adzitame mwa Yehova.”+ 2 Yohane 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aliyense amene amachita zosemphana ndi zimene Khristu amaphunzitsa,+ ndiye kuti akukana Mulungu.+ Koma amene amachita zinthu mogwirizana ndi zimene iye amaphunzitsa, amavomerezedwa ndi Atate ndiponso Mwana.+ 3 Yohane 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndinalemba nkhani inayake kumpingo, koma Diotirefe, amene amakonda kukhala woyamba+ pakati pawo, salandira mwaulemu+ chilichonse chochokera kwa ife.+
9 Aliyense amene amachita zosemphana ndi zimene Khristu amaphunzitsa,+ ndiye kuti akukana Mulungu.+ Koma amene amachita zinthu mogwirizana ndi zimene iye amaphunzitsa, amavomerezedwa ndi Atate ndiponso Mwana.+
9 Ndinalemba nkhani inayake kumpingo, koma Diotirefe, amene amakonda kukhala woyamba+ pakati pawo, salandira mwaulemu+ chilichonse chochokera kwa ife.+