Genesis 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pambuyo pake, Abulahamu anapatsa Isaki zonse zimene anali nazo.+ Aroma 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiponso si onse amene ali ana chifukwa chongokhala mbewu ya Abulahamu.+ Koma Malemba amati, “Amene adzatchedwa ‘mbewu yako’ adzachokera mwa Isaki.”+ Aroma 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Izi zikutanthauza kuti, si ana akuthupi+ amene alidi ana a Mulungu,+ koma ana a lonjezo+ ndiwo amayesedwa mbewu.
7 Ndiponso si onse amene ali ana chifukwa chongokhala mbewu ya Abulahamu.+ Koma Malemba amati, “Amene adzatchedwa ‘mbewu yako’ adzachokera mwa Isaki.”+
8 Izi zikutanthauza kuti, si ana akuthupi+ amene alidi ana a Mulungu,+ koma ana a lonjezo+ ndiwo amayesedwa mbewu.