1 Yohane 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Onse amene ali ana+ a Mulungu amagonjetsa dziko.+ Ndipo tagonjetsa+ dziko ndi chikhulupiriro chathu.+ Chivumbulutso 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Wopambana pa nkhondo+ ndidzamulola kukhala nane pampando wanga wachifumu,+ monga mmene ine ndinakhalira+ ndi Atate wanga pampando wawo wachifumu+ nditapambana pa nkhondo.
4 Onse amene ali ana+ a Mulungu amagonjetsa dziko.+ Ndipo tagonjetsa+ dziko ndi chikhulupiriro chathu.+
21 Wopambana pa nkhondo+ ndidzamulola kukhala nane pampando wanga wachifumu,+ monga mmene ine ndinakhalira+ ndi Atate wanga pampando wawo wachifumu+ nditapambana pa nkhondo.