Maliko 9:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Mchere ndi wabwino, koma mcherewo ukatha mphamvu, kodi mungaibwezeretse bwanji?+ Khalani ndi mchere+ mwa inu nokha, ndipo sungani mtendere+ pakati panu.” 2 Akorinto 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pomalizira abale, ndikuti pitirizani kukondwera, kusintha maganizo anu, kulimbikitsidwa,+ kukhala ndi maganizo ogwirizana,+ ndiponso kukhala mwamtendere.+ Mukatero, Mulungu wachikondi ndi wamtendere+ adzakhala nanu. Aheberi 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yesetsani kukhala pa mtendere ndi anthu onse,+ komanso yesetsani kukhala oyera+ chifukwa ngati munthu si woyera, sadzaona Ambuye.+ 1 Petulo 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 koma aleke zoipa+ ndipo achite zabwino. Ayesetse kupeza mtendere ndi kuusunga.+
50 Mchere ndi wabwino, koma mcherewo ukatha mphamvu, kodi mungaibwezeretse bwanji?+ Khalani ndi mchere+ mwa inu nokha, ndipo sungani mtendere+ pakati panu.”
11 Pomalizira abale, ndikuti pitirizani kukondwera, kusintha maganizo anu, kulimbikitsidwa,+ kukhala ndi maganizo ogwirizana,+ ndiponso kukhala mwamtendere.+ Mukatero, Mulungu wachikondi ndi wamtendere+ adzakhala nanu.
14 Yesetsani kukhala pa mtendere ndi anthu onse,+ komanso yesetsani kukhala oyera+ chifukwa ngati munthu si woyera, sadzaona Ambuye.+