Aroma 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 N’zoonadi! Iwo anadulidwa chifukwa chakuti analibe chikhulupiriro,+ koma iweyo waimirira chifukwa cha chikhulupiriro.+ Taya maganizo odzikuzawo,+ koma khala ndi mantha.+ 1 Akorinto 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsopano abale, ndikukuuzani uthenga wabwino+ umene ndinaulengeza kwa inu,+ umenenso munaulandira, ndiponso umene mwakhazikikamo.+ Afilipi 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho abale anga okondedwa, inu amene ndimakukondani ndiponso amene ndimalakalaka kukuonani, inu chimwemwe changa ndi chisoti changa chaulemerero,+ pitirizani kulimbikira+ mwa Ambuye.
20 N’zoonadi! Iwo anadulidwa chifukwa chakuti analibe chikhulupiriro,+ koma iweyo waimirira chifukwa cha chikhulupiriro.+ Taya maganizo odzikuzawo,+ koma khala ndi mantha.+
15 Tsopano abale, ndikukuuzani uthenga wabwino+ umene ndinaulengeza kwa inu,+ umenenso munaulandira, ndiponso umene mwakhazikikamo.+
4 Choncho abale anga okondedwa, inu amene ndimakukondani ndiponso amene ndimalakalaka kukuonani, inu chimwemwe changa ndi chisoti changa chaulemerero,+ pitirizani kulimbikira+ mwa Ambuye.