1 Akorinto 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Alipo kodi msilikali amene amatumikira, koma n’kumadzilipira yekha? Ndani amalima munda wa mpesa koma osadya zipatso zake?+ Kapena ndani amaweta ziweto koma osamwako mkaka wake?+ 1 Akorinto 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kapena kodi mawu amenewo kwenikweni akunenera ife? Ndithudi, mawu amenewo analembera ife,+ chifukwa wolima ayenera kulima ndi chiyembekezo ndipo munthu wopuntha mbewu azipuntha ndi chiyembekezo chodzadya nawo.+
7 Alipo kodi msilikali amene amatumikira, koma n’kumadzilipira yekha? Ndani amalima munda wa mpesa koma osadya zipatso zake?+ Kapena ndani amaweta ziweto koma osamwako mkaka wake?+
10 Kapena kodi mawu amenewo kwenikweni akunenera ife? Ndithudi, mawu amenewo analembera ife,+ chifukwa wolima ayenera kulima ndi chiyembekezo ndipo munthu wopuntha mbewu azipuntha ndi chiyembekezo chodzadya nawo.+